23 ndipo analowa, nakhalamo; koma sa namvera mau anu, sanayenda m'cilamulo canu; sanacita kanthu ka zonse zimene munawauza acite; cifukwa cace mwafikitsa pa iwo coipa conseci;
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 32
Onani Yeremiya 32:23 nkhani