43 Ndipo minda idzagulidwa m'dziko lino, limene muti, Ndilo bwinja, lopanda munthu kapena nyama; loperekedwa m'dzanja la Akasidi.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 32
Onani Yeremiya 32:43 nkhani