Yeremiya 33:18 BL92

18 ndiponso ansembe sadzasowa munthu pamaso panga wakupereka nsembe zopsereza, ndi kutentha nsembe zaufa, ndi wakucita nsembe masiku onse.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 33

Onani Yeremiya 33:18 nkhani