Yeremiya 34:11 BL92

11 koma pambuyo pace anabwerera, nabweza akapolo ace amuna ndi akazi, amene anawamasula, nawagonjetsanso akhale akapolo amuna ndi akazi;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 34

Onani Yeremiya 34:11 nkhani