Yeremiya 35:16 BL92

16 Pakuti monga ana a Yonadabu mwana wa Rekabu acita lamulo la kholo lao limene anawauza, koma anthu awa sanandimvera Ine.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 35

Onani Yeremiya 35:16 nkhani