Yeremiya 36:16 BL92

16 Ndipo panali, pamene anamva mau onse, anaopa nayang'anana wina ndi mnzace, nati kwa Baruki, Tidzamfotokozeratu mfumu mau awa onse.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 36

Onani Yeremiya 36:16 nkhani