Yeremiya 36:18 BL92

18 Ndipo Baruki anayankha iwo, Pakamwa pace anandichulira ine mau awa onse, ndipo ndinawalemba ndi inki m'bukumo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 36

Onani Yeremiya 36:18 nkhani