Yeremiya 38:1 BL92

1 Ndipo Sefatiya mwana wa Matani ndi Gedaliya mwana wa Pusuri, ndi Yukali mwana wa Selemiya, ndi Pasuri mwana wa Malikiya, anamva mau amene Yeremiya ananena ndi anthu onse, kuti,

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 38

Onani Yeremiya 38:1 nkhani