Yeremiya 38:12 BL92

12 Ndipo Ebedi-Meleki Mkusi anati kwa Yeremiya, Kulungatu zingwe ndi nsaruzi zotaya zakale ndi zansanza ndi kuzikwapatira. Ndipo Yeremiya anacita comweco.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 38

Onani Yeremiya 38:12 nkhani