Yeremiya 39:14 BL92

14 iwonso anatumiza, namcotsa Yeremiya m'bwalo la kaidi, nampereka iye kwa Gedaliya mwana wa Ahikamu, mwana wa Safani, kuti anke naye kwao; momwemo iye anakhala ndi anthu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 39

Onani Yeremiya 39:14 nkhani