14 Iwe Yerusalemu, utsuke mtima wako kucotsa zoipa kuti upulumuke. Maganizo ako acabe agona mwako masiku angati?
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 4
Onani Yeremiya 4:14 nkhani