Yeremiya 4:2 BL92

2 Ndipo udzalumbira, Pali Yehova m'zoonadi, m'ciweruziro, ndi m'cilungamo; ndipo mitundu ya anthu idzadzidalitsa mwa Iye, ndipo mwa Iye adzatamandira.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 4

Onani Yeremiya 4:2 nkhani