Yeremiya 4:22 BL92

22 Pakuti anthu anga apusa, sandidziwa Ine; ali ana opulukira sazindikira; ali ocenjera kucita coipa koma kucita cabwino sakudziwa.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 4

Onani Yeremiya 4:22 nkhani