29 Mudzi wonse uthawa m'phokoso la apakavalo ndi amauta; adzalowa m'nkhalango, adzakwera pamiyala; midzi yonse idzasiyidwa, ndipo simudzakhala munthu m'menemo.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 4
Onani Yeremiya 4:29 nkhani