Yeremiya 4:6 BL92

6 Kwezani mbendera kuyang'ana ku Ziyoni; thawani kuti mupulumuke, musakhale; pakuti ndidza ndi coipa cocokera kumpoto ndi kuononga kwakukuru.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 4

Onani Yeremiya 4:6 nkhani