3 ndipo Yehova wacitengera, ndi kucita monga ananena, cifukwa mwacimwira Yehova, ndi kusamvera mau ace, cifukwa cace cinthu ici cakufikirani.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 40
Onani Yeremiya 40:3 nkhani