Yeremiya 41:13 BL92

13 Ndipo panali pamene anthu onse amene anali ndi Ismayeli anaona Yohanani mwana wa Kareya, ndi akazembe onse a nkhondo okhala naye, anasekera.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 41

Onani Yeremiya 41:13 nkhani