11 Musaope mfumu ya ku Babulo, amene mumuopa; musamuope, ati Yehova: pakuti Ine ndiri ndi inu kukupulumutsani, ndi kukulanditsani m'dzanja lace.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 42
Onani Yeremiya 42:11 nkhani