15 cifukwa cace mumve mau a Yehova, Otsala inu a Yuda, atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli, Ngati mulozetsa nkhope zanu kuti mulowe m'Aigupto, kukakhala m'menemo;
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 42
Onani Yeremiya 42:15 nkhani