Yeremiya 43:3 BL92

3 koma Baruki mwana wace wa Neriya aticicizira inu, mutipereke m'dzanja la Akasidi, kuti atiphe ife, atitengere ife am'nsinga ku Babulo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 43

Onani Yeremiya 43:3 nkhani