5 Koma Yohanani mwana wace wa Kareya, ndi akazembe onse: a nkhondo, anatenga otsala onse a Yuda, amene anabwera ku mitundu yonse kumene anaingitsidwirako kuti akhale m'dziko la Yuda;
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 43
Onani Yeremiya 43:5 nkhani