Yeremiya 45:3 BL92

3 Munati, Kalanga ine tsopano! pakuti Yehova waonjezera cisoni pa zowawa zanga; ndalema ndi kubuula kwanga, sindipeza kupuma,

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 45

Onani Yeremiya 45:3 nkhani