12 Amitundu amva manyazi anu, dziko lapansi ladzala ndi kupfuula kwanu; pakuti amphamvu akhumudwitsana, agwa onse awiri pamodzi.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 46
Onani Yeremiya 46:12 nkhani