16 Anapunthwitsa ambiri, inde, anagwa wina pa mnzace, ndipo anati, Ukani, tinkenso kwa anthu athu, ku dziko la kubadwa kwathu, kucokera ku lupanga lobvutitsa.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 46
Onani Yeremiya 46:16 nkhani