Yeremiya 46:19 BL92

19 Mwana wamkazi iwe wokhala m'Aigupto, dzikonzere kunka kundende; pakuti Nofi adzakhala bwinja, nadzapsya, mulibenso wokhalamo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 46

Onani Yeremiya 46:19 nkhani