4 Mangani akavalo, bwerani, inu apakavalo, imani ndi zisoti zacitsulo; tuulani nthungo zanu, bvalani malaya acitsulo.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 46
Onani Yeremiya 46:4 nkhani