Yeremiya 48:1 BL92

1 Za Moabu Atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli: Tsoka Nebo! pakuti wapasuka; Kiriyataimu wacitidwa manyazi, wagwidwa; linga la pamtunda lacitidwa manyazi lapasudwa.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 48

Onani Yeremiya 48:1 nkhani