11 Moabu wakhala m'mtendere kuyambira ubwana wace, wakhala pansenga, osatetekulidwa, sananke kundende; cifukwa cace makoleredwe ace alimobe mwa iye, pfungo lace silinasinthika.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 48
Onani Yeremiya 48:11 nkhani