Yeremiya 48:26 BL92

26 Umledzeretse iye; pakuti anadzikuza pokana Yehova; Moabu yemwe adzabvimvinika m'kusanza kwace, ndipo iye adzasekedwanso.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 48

Onani Yeremiya 48:26 nkhani