36 Cifukwa cace mtima wanga umlima Moabu monga zitolilo, ndipo mtima wanga uwalirira anthu a Kireresi monga zitolilo, cifukwa cace zakucuruka zace adadzionera zatayika.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 48
Onani Yeremiya 48:36 nkhani