Yeremiya 48:44 BL92

44 Ndipo iye wakuthawa cifukwa ca mantha adzagwa m'dzenje; ndi iye amene aturuka m'dzenje adzagwidwa m'khwekhwe; pakuti ndidzatengera pa iye, pa Moabu, caka ca kulangidwa kwao, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 48

Onani Yeremiya 48:44 nkhani