1 Za ana a Amoni. Yehova atero: Kodi Israyeli alibe ana amuna? alibe wolowa dzina? M'mwemo mfumu yao yalowa pa Gadi cifukwa canji, ndi anthu ace akhala m'midzi mwace?
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 49
Onani Yeremiya 49:1 nkhani