Yeremiya 49:11 BL92

11 Siya ana ako amasiye, Ine ndidzawasunga; akazi ako amasiye andikhulupirire Ine.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 49

Onani Yeremiya 49:11 nkhani