Yeremiya 49:18 BL92

18 Monga m'kupasuka kwa Sodomu ndi Gomora ndi midzi inzace, ati Yehova, munthu ali yense sadzakhala m'menemo, mwana wa munthu ali yense sadzagona m'menemo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 49

Onani Yeremiya 49:18 nkhani