23 Za Damasiko. Hamati ndi Aripadi ali ndi manyazi, cifukwa anamva malodza, asungunuka kunyanja, adera nkhawa osatha kukhala cete.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 49
Onani Yeremiya 49:23 nkhani