Yeremiya 49:26 BL92

26 Cifukwa cace anyamata ace adzagwa m'miseu yace, ndipo anthu onse a nkhondo adzatontholetsedwa tsiku lomwelo, ati Yehova wa makamu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 49

Onani Yeremiya 49:26 nkhani