24 Ndipo sanena m'mtima mwao, Tiopetu Yehova Mulungu wathu wopatsa mvula yoyamba ndi yamasika, m'nyengo yace; atisungira ife masabata olamulidwa a masika.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 5
Onani Yeremiya 5:24 nkhani