Yeremiya 50:3 BL92

3 Pakuti mtundu wa anthu udzaturuka kumpoto kudzamenyana naye, udzacititsa dziko lace bwinja, losakhalamo anthu; athawa, apita, anthu ndi nyama.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50

Onani Yeremiya 50:3 nkhani