Yeremiya 50:37 BL92

37 Lupanga liri pa akavalo ao, ndi pa magareta ao, ndi pa anthu onse osanganizidwa amene ali pakati pace, ndipo adzakhala ngati akazi; lupanga liri pa cuma cace, ndipo cidzalandidwa.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50

Onani Yeremiya 50:37 nkhani