Yeremiya 50:40 BL92

40 Monga muja Yehova anagwetsa Sodomu ndi Gomora ndi midzi Inzace, ati Yehova; anthu sadzakhalamo, mwana wa munthu sadzagonamo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50

Onani Yeremiya 50:40 nkhani