43 Mfumu ya ku Babulo yamva mbiri yao, ndipo manja ace alefuka; wagwidwa ndi nkhawa, ndi zowawa zonga za mkazi alimkudwala.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50
Onani Yeremiya 50:43 nkhani