19 Gawo la Yakobo silifanafana ndi izo; pakuti Iye ndiye analenga zonse; Israyeli ndi mtundu wa colowa cace, dzina lace ndi Yehova wa makamu.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 51
Onani Yeremiya 51:19 nkhani