26 Ndipo sadzacotsa pa iwe mwala wa pangondya, kapena mwala wa pamaziko; koma udzakhala bwinja nthawi zonse, ati Yehova.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 51
Onani Yeremiya 51:26 nkhani