Yeremiya 51:28 BL92

28 Konzerani amitundu amenyane ndi iye, mafumu a Amedi, akazembe ace, ndi ziwanga zace zonse, ndi dziko lonse la ufumu wace.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 51

Onani Yeremiya 51:28 nkhani