Yeremiya 51:33 BL92

33 Pakuti atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli: Mwana wamkazi wa Babulo akunga dwale pamene aliunda; patsala kanthawi kakang'ono, ndipo nthawi yamasika idzamfikira iye.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 51

Onani Yeremiya 51:33 nkhani