44 Ndipo Ine ndiweruza Beli m'Babulo, ndipo ndidzaturutsa m'kamwa mwace comwe wacimeza; ndipo amitundu sadzasonkhaniranso konse kwa iye; inde, khoma la Babulo lidzagwa.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 51
Onani Yeremiya 51:44 nkhani