Yeremiya 51:47 BL92

47 Cifukwa cace, taonani, masiku alinkudza, amene ndidzaweruza mafano osemasema a Babulo, ndipo dziko lace lonse lidzakhala ndi manyazi; ndipo ophedwa ace onse adzagwa pakati pace.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 51

Onani Yeremiya 51:47 nkhani