Yeremiya 52:10 BL92

10 Ndipo mfumu ya ku Babulo inapha ana a Zedekiya pamaso pace; niphanso akuru onse a Yuda m'Ribila.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 52

Onani Yeremiya 52:10 nkhani