Yeremiya 52:3 BL92

3 Pakuti zonse zinacitika m'Yerusalemu ndi m'Yuda cifukwa ca mkwiyo wa Yehova, mpaka anawacotsa pamaso pace; ndipo Zedekiya anampandukira mfumu ya Babulo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 52

Onani Yeremiya 52:3 nkhani