Yeremiya 6:12 BL92

12 Nyumba zao zidzasanduka za ena, pamodzi ndi minda yao ndi akazi ao; pakuti ndidzatambasula dzanja langa pa okhala m'dziko, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 6

Onani Yeremiya 6:12 nkhani